Revision 34219 of "Mukondo Chileshe" on nywiki

Mukondo Chileshe ndi woimba wa ku Zambia yemwe amasewera ndi dzina la Muki. Wagwira ntchito limodzi ndi woimba wa Ku kenya monga Ian Magoma.